Salimo 109:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikawachitira zabwino iwo amandibwezera zoipa+Ndikawasonyeza chikondi amadana nane.+