-
Yobu 2:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Patapita nthawi, mkazi wake anamufunsa kuti: “Kodi mukupitirizabe kukhala wokhulupirika? Tukwanani Mulungu mufe!” 10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa. Kodi tizingolandira zabwino zokhazokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ Ngakhale kuti anakumana ndi zonsezi, Yobu sananene chilichonse cholakwika.*+
-