Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa zikondwerero zawo amaimbapo azeze, zoimbira za zingwe,

      Maseche ndi zitoliro ndipo amamwapo vinyo.

      Koma saganizira zochita za Yehova,

      Ndipo saona ntchito ya manja ake.

  • Yesaya 22:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma mʼmalomwake mukukondwera ndi kusangalala,

      Mukupha ngʼombe ndi nkhosa,

      Mukudya nyama ndi kumwa vinyo.+

      Inu mukuti, ‘Tiyeni tidye ndi kumwa, chifukwa mawa tifa.’”+

  • Amosi 6:4, 5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Mumagona pamabedi aminyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamipando yokhala ngati bedi,+

      Ndiponso mukudya nkhosa zamphongo komanso ana a ngʼombe* onenepa.+

       5 Mumapeka nyimbo zoti muziimba ndi zeze,*+

      Ndipo mofanana ndi Davide, mumapanga zipangizo zoimbira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena