Miyambo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala kwa nyale ya anthu olungama kukuwonjezeka kwambiri.*+Koma nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+ Miyambo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense amene amatemberera bambo ake komanso mayi ake,Nyale yake idzazimitsidwa kukagwa mdima.+ Miyambo 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa aliyense woipa alibe tsogolo,+Ndipo nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+
9 Kuwala kwa nyale ya anthu olungama kukuwonjezeka kwambiri.*+Koma nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+