Salimo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo. Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezedwa, koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona kuti mumakonda kwambiri anthu anu* ndipo adzachita manyazi. Inde, moto wanu udzapsereza adani anu.
6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo.
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezedwa, koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona kuti mumakonda kwambiri anthu anu* ndipo adzachita manyazi. Inde, moto wanu udzapsereza adani anu.