-
Mateyu 24:38, 39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Mʼmasiku amenewo Chigumula chisanafike, anthu ankadya ndi kumwa. Amuna ankakwatira ndipo akazi ankakwatiwa mpaka tsiku limene Nowa analowa mʼchingalawa.+ 39 Anthu ananyalanyaza zimene zinkachitika mpaka Chigumula chinafika nʼkuwaseseratu onsewo.+ Zidzakhalanso choncho ndi kukhalapo kwa Mwana wa munthu.
-