Yobu 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati ndinkaona munthu akuzunzika ndi mphepo chifukwa chosowa chovala,Kapena munthu wosauka akusowa chofunda,+ Yobu 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkono wanga ugwe* kuchoka mʼmalo mwake,Ndipo mkono wanga uthyoke pachigongono.*
19 Ngati ndinkaona munthu akuzunzika ndi mphepo chifukwa chosowa chovala,Kapena munthu wosauka akusowa chofunda,+ Yobu 31:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mkono wanga ugwe* kuchoka mʼmalo mwake,Ndipo mkono wanga uthyoke pachigongono.*