Deuteronomo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukadzalandira cholowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu musamadzasunthe zizindikiro za malire a mnzanu,+ pamalo amene makolo anu anaika kale malire. Deuteronomo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Wotembereredwa ndi munthu wosuntha chizindikiro cha malire a mnzake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’) Miyambo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usamasunthe chizindikiro chakalekale cha malire,+Kapena kulowerera munda wa ana amasiye. Hoseya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akalonga a Yuda ali ngati anthu osuntha malire.+ Ndidzawakhuthulira mkwiyo wanga ngati madzi.
14 Mukadzalandira cholowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale lanu musamadzasunthe zizindikiro za malire a mnzanu,+ pamalo amene makolo anu anaika kale malire.
17 ‘Wotembereredwa ndi munthu wosuntha chizindikiro cha malire a mnzake.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’)