8 Iye ankadutsa mumsewu pafupi ndi mphambano,
Ndipo ankalowera kunyumba ya mkaziyo
9 Pa nthawi yamadzulo kuli kachisisira,+
Kutatsala pangʼono kuda.
10 Kenako ndinaona mkazi akubwera kudzakumana naye,
Atavala ngati hule+ ndipo anali ndi mtima wachinyengo.