Yohane 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amene amachita zinthu zoipa amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisaonekere.*
20 Amene amachita zinthu zoipa amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisaonekere.*