Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 4:17, 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ‘Kodi munthu angakhale wolungama kuposa Mulungu?

      Kodi munthu angakhale woyera kuposa amene anamupanga?’

      18 Iyetu sakhulupirira atumiki ake,

      Ndipo angelo* ake amawapezera zifukwa.

  • Yobu 22:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Kodi zoti ndiwe wolungama, Wamphamvuyonse ali nazo ntchito?*

      Kapena kodi amapindula chilichonse chifukwa choti umachita zinthu mokhulupirika?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena