Genesis 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehova anati: “Bwanji ndimuuze Abulahamu zimene ndikufuna kuchita?+ Genesis 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake zonse* kuyenda mʼnjira ya Yehova. Azichita zimenezi pochita zabwino ndi zachilungamo+ kuti Yehova adzakwaniritse zimene ananena zokhudza Abulahamu.”
19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake zonse* kuyenda mʼnjira ya Yehova. Azichita zimenezi pochita zabwino ndi zachilungamo+ kuti Yehova adzakwaniritse zimene ananena zokhudza Abulahamu.”