Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu? Padziko lapansi palibe wina wofanana naye. Iye ndi munthu wokhulupirika amene amachita zoyenera,*+ amaopa Mulungu ndiponso amapewa zoipa. Iye akupitirizabe kukhala wokhulupirika+ ngakhale kuti iweyo ukufuna kuti ndimuwononge*+ popanda chifukwa.”

  • Yobu 27:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Inetu sindingayerekeze nʼkomwe kunena kuti amuna inu ndinu olungama.

      Mpaka ndidzamwalire, sindidzasiya* kukhala wokhulupirika.+

  • Salimo 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova adzapereka chigamulo kwa mitundu ya anthu.+

      Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa

      Komanso mogwirizana ndi kukhulupirika kwanga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena