Genesis 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kudothi,*+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ mumphuno mwake, munthuyo nʼkukhala wamoyo.+ Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+ Machitidwe 17:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo, mpweya+ ndi zinthu zonse.
7 Kenako Yehova Mulungu anaumba munthu kuchokera kudothi,*+ ndipo anauzira mpweya wa moyo+ mumphuno mwake, munthuyo nʼkukhala wamoyo.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+
25 Komanso satumikiridwa ndi manja a anthu ngati kuti amasowa kanthu,+ chifukwa ndi iyeyo amene amapatsa anthu onse moyo, mpweya+ ndi zinthu zonse.