Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu mukudziwa kuti ndine wosalakwa,+

      Ndipo palibe amene angandipulumutse mʼmanja mwanu.+

  • Yobu 16:16, 17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Nkhope yanga yafiira chifukwa cholira,+

      Ndipo pazikope zanga pali mdima wandiweyani,*

      17 Ngakhale kuti manja anga sanachite zachiwawa,

      Ndipo pemphero langa ndi loyera.

  • Yobu 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mapazi anga akuponda mmene mapazi ake akuponda.

      Ndapitiriza kuyenda mʼnjira yake ndipo sindinapatuke.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena