Yobu 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Iye adzabwera nthawi ina ndipo adzaimirira padziko lapansi.* Mateyu 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+
25 Ine ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Iye adzabwera nthawi ina ndipo adzaimirira padziko lapansi.*
28 Izi zikufanana ndi zimene Mwana wa munthu anachita. Iye sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+