Salimo 68:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+ Ulemerero wake uli pa Isiraeli,Ndipo amasonyeza mphamvu zake kuchokera kumwamba.*
34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu zochuluka.+ Ulemerero wake uli pa Isiraeli,Ndipo amasonyeza mphamvu zake kuchokera kumwamba.*