Salimo 42:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masana Yehova adzandisonyeza chikondi chake chokhulupirika,Ndipo usiku ndidzamuimbira nyimbo, ndidzapemphera kwa Mulungu amene amandipatsa moyo.+ Salimo 149:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu okhulupirika asangalale chifukwa Mulungu amawalemekeza.Iwo aimbe mosangalala ali pamabedi awo.+ Machitidwe 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma chapakati pa usiku, Paulo ndi Sila anayamba kupemphera ndiponso kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ moti akaidi ena ankawamva.
8 Masana Yehova adzandisonyeza chikondi chake chokhulupirika,Ndipo usiku ndidzamuimbira nyimbo, ndidzapemphera kwa Mulungu amene amandipatsa moyo.+
5 Anthu okhulupirika asangalale chifukwa Mulungu amawalemekeza.Iwo aimbe mosangalala ali pamabedi awo.+
25 Koma chapakati pa usiku, Paulo ndi Sila anayamba kupemphera ndiponso kutamanda Mulungu poimba nyimbo,+ moti akaidi ena ankawamva.