Miyambo 1:28, 29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.Adzayesetsa kundifunafuna koma sadzandipeza,+29 Chifukwa chakuti anadana ndi kudziwa zinthu,+Ndipo sanasankhe kuopa Yehova.+ 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
28 Pa nthawi imeneyo azidzangondiitana koma sindidzayankha.Adzayesetsa kundifunafuna koma sadzandipeza,+29 Chifukwa chakuti anadana ndi kudziwa zinthu,+Ndipo sanasankhe kuopa Yehova.+
5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+