Yobu 34:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 ‘Yobu sadziwa zimene akunena,+Ndipo mawu ake amasonyeza kuti ndi wosazindikira.’ Yobu 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi uyu ndi ndani amene akuphimba malangizo angayuNʼkumalankhula mopanda nzeru?+