Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa Yehova ndi wolungama.+ Iye amakonda ntchito zolungama.+ Anthu owongoka mtima adzaona nkhope yake.*+ Salimo 139:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndimakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa+ ndipo zimenezi zimandichititsa mantha. Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ine ndikudziwa bwino zimenezi. Danieli 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma inu Yehova, munakhala tcheru ndipo munatigwetsera tsoka chifukwa inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+ Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+ Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita zinthu zopanda chilungamo.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
7 Chifukwa Yehova ndi wolungama.+ Iye amakonda ntchito zolungama.+ Anthu owongoka mtima adzaona nkhope yake.*+
14 Ndimakutamandani chifukwa munandipanga modabwitsa+ ndipo zimenezi zimandichititsa mantha. Ntchito zanu ndi zodabwitsa,+Ine ndikudziwa bwino zimenezi.
14 Koma inu Yehova, munakhala tcheru ndipo munatigwetsera tsoka chifukwa inu Yehova Mulungu wathu ndinu wolungama pa ntchito zonse zimene mwachita, koma ife sitinamvere mawu anu.+
3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+