Salimo 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndi ndani? Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova, wamphamvu pankhondo.+ Salimo 99:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi mfumu yamphamvu imene imakonda chilungamo.+ Nthawi zonse mumaonetsetsa kuti chilungamo chachitika. Mwabweretsa chiweruzo cholungama komanso chilungamo+ pakati pa ana a Yakobo. Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu amene mumasonyeza anthu masauzande ambiri chikondi chokhulupirika koma mumabwezera kwa ana,* zolakwa za abambo awo.+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu ndi wamphamvu ndipo dzina lanu ndinu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
8 Kodi Mfumu yaulemerero imeneyi ndi ndani? Ndi Yehova, wanyonga ndi wamphamvu,+Yehova, wamphamvu pankhondo.+
4 Iye ndi mfumu yamphamvu imene imakonda chilungamo.+ Nthawi zonse mumaonetsetsa kuti chilungamo chachitika. Mwabweretsa chiweruzo cholungama komanso chilungamo+ pakati pa ana a Yakobo.
18 Inu amene mumasonyeza anthu masauzande ambiri chikondi chokhulupirika koma mumabwezera kwa ana,* zolakwa za abambo awo.+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu ndi wamphamvu ndipo dzina lanu ndinu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.