Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa adzapita ku Manda,*Anthu a mitundu yonse amene aiwala Mulungu adzapita kumeneko. Salimo 68:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi mphepo imene imathamangitsa utsi, inunso muwathamangitsire kutali.Mofanana ndi phula limene limasungunuka pamoto,Anthu oipa awonongeke pamaso pa Mulungu.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+
2 Mofanana ndi mphepo imene imathamangitsa utsi, inunso muwathamangitsire kutali.Mofanana ndi phula limene limasungunuka pamoto,Anthu oipa awonongeke pamaso pa Mulungu.+
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+