Miyambo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma anthu oipa adzachotsedwa padziko lapansi+Ndipo achinyengo adzazulidwamo.+ Yeremiya 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi,Chifukwa Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu. Iye adzapereka yekha chiweruzo kwa anthu onse.+ Ndipo anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’ akutero Yehova.
31 ‘Phokoso lidzamveka kumalekezero a dziko lapansi,Chifukwa Yehova akufuna kuimba mlandu mitundu ya anthu. Iye adzapereka yekha chiweruzo kwa anthu onse.+ Ndipo anthu oipa adzawapha ndi lupanga,’ akutero Yehova.