Yobu 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo angafe mwadzidzidzi,+ pakati pa usiku.+Amaphupha nʼkufa.Ngakhale anthu amphamvu amawonongedwa, koma osati ndi manja a anthu.+ Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+ Miyambo 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+
20 Iwo angafe mwadzidzidzi,+ pakati pa usiku.+Amaphupha nʼkufa.Ngakhale anthu amphamvu amawonongedwa, koma osati ndi manja a anthu.+
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
4 Chuma chidzakhala chopanda* phindu pa tsiku la mkwiyo woopsa,+Koma chilungamo nʼchimene chidzapulumutse munthu ku imfa.+