Salimo 92:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ntchito zanu ndi zazikulu kwambiri inu Yehova!+ Maganizo anu ndi ozama kwambiri.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+ Zonsezo munazipanga mwanzeru.+ Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.