Yobu 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amamveka pansi ponse pa thambo,Ndipo amatumiza mphezi yake+ kumalekezero a dziko lapansi.