2 Samueli 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anaponya mivi yake+ ndipo anawabalalitsa;Anaponya mphezi ndipo anawasokoneza.+ Salimo 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anaponya mivi yake nʼkuwabalalitsa.+Anaponya mphezi zake nʼkuwachititsa kuti asokonezeke.+ Salimo 144:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chititsani kuti mphezi zingʼanime kuti adani abalalike.+Ponyani mivi yanu ndipo muwasokoneze.+