Zekariya 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula pa nthawi ya mvula yomalizira. Yehova ndi amene amapanga mitambo yamvula,Ndiponso amene amagwetsera anthu mvula.+Iye amakulitsa mbewu mʼmunda mwa munthu aliyense.
10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula pa nthawi ya mvula yomalizira. Yehova ndi amene amapanga mitambo yamvula,Ndiponso amene amagwetsera anthu mvula.+Iye amakulitsa mbewu mʼmunda mwa munthu aliyense.