Salimo 104:25, 26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pali nyanja, yomwe ndi yakuya komanso yaikulu kwambiri,Mmene muli zamoyo zosawerengeka, zazikulu ndi zazingʼono zomwe.+ 26 Sitima zimayenda mmenemo,Ndipo Leviyatani*+ munamupanga kuti azisewera mmenemo.
25 Pali nyanja, yomwe ndi yakuya komanso yaikulu kwambiri,Mmene muli zamoyo zosawerengeka, zazikulu ndi zazingʼono zomwe.+ 26 Sitima zimayenda mmenemo,Ndipo Leviyatani*+ munamupanga kuti azisewera mmenemo.