Yesaya 41:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.
15 “Taona! Ndakusandutsa chopunthira mbewu,+Chida chatsopano chopunthira mbewu chokhala ndi mano akuthwa konsekonse. Udzapondaponda mapiri nʼkuwaphwanyaNdipo zitunda udzazisandutsa mankhusu.