Yobu 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nʼchifukwa chiyani oipa amakhalabe ndi moyo,+Amakalamba komanso amalemera* kwambiri?+ Yobu 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma iwo amauza Mulungu woona kuti, ‘Tisiyeni! Sitikufuna kudziwa njira zanu.+