19 Kenako amuna a ku Zifi anapita kwa Sauli ku Gibeya+ nʼkumuuza kuti: “Davide akubisalatu pafupi ndi ife+ kumalo ovuta kufikako ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ lomwe lili kumʼmwera* kwa Yesimoni.*+
26Patapita nthawi, amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Davide akubisala kuphiri la Hakila mbali imene yayangʼanizana ndi Yesimoni.”*+