Salimo 69:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ine ndavutika ndipo ndikumva ululu.+ Inu Mulungu, mundipulumutse komanso munditeteze.