Mlaliki 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndaonanso zinthu izi padziko lapansi pano: Pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+ Mika 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya YakoboKomanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+Amene mumadana ndi chilungamo ndiponso mumapotoza zinthu zonse zowongoka,+
16 Ine ndaonanso zinthu izi padziko lapansi pano: Pamene panayenera kukhala chilungamo panali zoipa, ndipo pamene panayenera kuchitika zachilungamo panachitika zoipa.+
9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya YakoboKomanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+Amene mumadana ndi chilungamo ndiponso mumapotoza zinthu zonse zowongoka,+