Miyambo 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mphepo yamkuntho ikawomba woipa amawonongedwa,+Koma wolungama ali ngati maziko mpaka kalekale.+ Yeremiya 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Mkwiyo wa Yehova udzawomba ngati mphepo yamkuntho.Udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu pamitu ya anthu oipa.+
19 Taonani! Mkwiyo wa Yehova udzawomba ngati mphepo yamkuntho.Udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu pamitu ya anthu oipa.+