Miyambo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa ndi dipo la munthu wolungama,Ndipo munthu wochita zachinyengo adzatengedwa mʼmalo mwa anthu owongoka mtima.+
18 Munthu woipa ndi dipo la munthu wolungama,Ndipo munthu wochita zachinyengo adzatengedwa mʼmalo mwa anthu owongoka mtima.+