2 Samueli 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso Davide anatchuka kwambiri atabwerako kumene anakapha Aedomu 18,000 mʼchigwa cha Mchere.+ 1 Mbiri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide anagonjetsa Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ pafupi ndi Hamati,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kukakhazikitsa ulamuliro wake kumtsinje wa Firate.+
3 Davide anagonjetsa Hadadezeri+ mfumu ya Zoba+ pafupi ndi Hamati,+ pamene Hadadezeriyo ankapita kukakhazikitsa ulamuliro wake kumtsinje wa Firate.+