Yesaya 51:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+Iwe amene wamwa zinthu zamʼkapu ya mkwiyo wa Yehova kuchokera mʼdzanja lake. Iweyo wamwa zimene zili mʼchipanda,Wagugudiza kapu yochititsa kuti munthu aziyenda dzandidzandi.+
17 Dzuka! Dzuka! Imirira iwe Yerusalemu,+Iwe amene wamwa zinthu zamʼkapu ya mkwiyo wa Yehova kuchokera mʼdzanja lake. Iweyo wamwa zimene zili mʼchipanda,Wagugudiza kapu yochititsa kuti munthu aziyenda dzandidzandi.+