Deuteronomo 1:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma Yehova anandiuza kuti, ‘Auze kuti: “Musapite kukamenya nkhondo, chifukwa ine sindikhala nanu.+ Mukapita, adani anu akakugonjetsani.”’ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+ Yoswa 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+
42 Koma Yehova anandiuza kuti, ‘Auze kuti: “Musapite kukamenya nkhondo, chifukwa ine sindikhala nanu.+ Mukapita, adani anu akakugonjetsani.”’
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda nanu limodzi kuti akumenyereni nkhondo nʼkukupulumutsani kwa adani anu.’+
12 Choncho Aisiraeli sadzathanso kulimbana ndi adani awo. Iwo azingogonja nʼkumathawa adani awo, chifukwa nawonso akhala zinthu zoyenera kuwonongedwa. Sindikhalanso nanu kufikira mutachotsa pakati panu zinthu zoyenera kuwonongedwazo.+