Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+ Salimo 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, mfumu ikusangalala chifukwa mwasonyeza kuti ndinu wamphamvu.+Ikusangalala kwambiri chifukwa mwaipulumutsa.+ Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo wautali ndipo munaipatsadi.+Munaipatsa moyo wautali* kuti ikhale mpaka kalekale.
50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+
21 Inu Yehova, mfumu ikusangalala chifukwa mwasonyeza kuti ndinu wamphamvu.+Ikusangalala kwambiri chifukwa mwaipulumutsa.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo wautali ndipo munaipatsadi.+Munaipatsa moyo wautali* kuti ikhale mpaka kalekale.