2 Samueli 7:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 17 Natani anauza Davide mawu onsewa ndiponso masomphenya onse amene anaona.+ Salimo 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+
16 Nyumba yako ndi ufumu wako zidzakhalapobe mpaka kalekale. Mpando wako wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.”’”+ 17 Natani anauza Davide mawu onsewa ndiponso masomphenya onse amene anaona.+
12 Koma ine mumandithandiza chifukwa choti ndine wokhulupirika,+Ndipo mudzasangalala nane mpaka kalekale.*+