1 Mbiri 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu mabanja a mitundu ya anthu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+ Salimo 96:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene amakhala pali ulemu ndi ulemerero.+Mphamvu ndi kukongola zili mʼnyumba yake yopatulika.+
28 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu mabanja a mitundu ya anthu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+