Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anthu onse amene amathawira kwa inu adzasangalala.+

      Nthawi zonse adzafuula mosangalala.

      Inu mudzawateteza kuti anthu oipa asawafikire,

      Ndipo anthu okonda dzina lanu adzasangalala chifukwa cha inu.

  • Salimo 57:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 57 Ndikomereni mtima inu Mulungu, ndikomereni mtima,

      Chifukwa ine ndathawira kwa inu.+

      Ndathawira mumthunzi wa mapiko anu mpaka mavuto atadutsa.+

  • Salimo 61:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndidzakhala mlendo mutenti yanu mpaka kalekale.+

      Ndidzabisala mumthunzi wa mapiko anu.+ (Selah)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena