Salimo 7:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu ndi Woweruza wolungama,+Ndipo Mulungu amapereka zigamulo kwa* oipa tsiku lililonse. 12 Ngati munthu sakulapa,+ Mulungu amanola lupanga lake,+Amakunga uta wake nʼkukonzekera kulasa.+
11 Mulungu ndi Woweruza wolungama,+Ndipo Mulungu amapereka zigamulo kwa* oipa tsiku lililonse. 12 Ngati munthu sakulapa,+ Mulungu amanola lupanga lake,+Amakunga uta wake nʼkukonzekera kulasa.+