Salimo 107:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mulungu amachititsa manyazi anthu olemekezekaNdipo amawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu mmene mulibe njira.+ Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Aliyense wanzeru aona zinthu zimenezi+Ndipo aganizira mofatsa zimene Yehova wachita posonyeza chikondi chake chokhulupirika.+
40 Mulungu amachititsa manyazi anthu olemekezekaNdipo amawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu mmene mulibe njira.+
43 Aliyense wanzeru aona zinthu zimenezi+Ndipo aganizira mofatsa zimene Yehova wachita posonyeza chikondi chake chokhulupirika.+