Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake.

  • Salimo 85:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndithudi, Yehova adzapereka zinthu zabwino,*+

      Ndipo dziko lathu lidzapereka zokolola zake.+

  • Yesaya 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+

  • Ezekieli 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mitengo yamʼdzikomo idzabereka zipatso ndipo nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala mʼdzikolo motetezeka ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzathyola goli lawo+ nʼkuwapulumutsa kwa anthu amene anawagwira kuti akhale akapolo awo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena