Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho Yehova anamva mawu a Aisiraeli ndipo anapereka Akananiwo mʼmanja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. Nʼchifukwa chake malowo anawatchula kuti Horima.*+

  • Yoswa 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho mafumu 5 a Aamoriwo,+ limodzi ndi magulu awo ankhondo, anasonkhana pamodzi ndipo anakamanga msasa pafupi ndi anthu a ku Gibiyoni nʼcholinga choti amenyane nawo. Mafumuwo anali mfumu ya ku Yerusalemu, mfumu ya ku Heburoni, mfumu ya ku Yarimuti, mfumu ya ku Lakisi ndi mfumu ya ku Egiloni.

  • Yoswa 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova anasokoneza adaniwo pamaso pa Aisiraeli.+ Ndipo Aisiraeli anapha adani ambirimbiri ku Gibiyoni. Anawathamangitsa kulowera kuchitunda cha Beti-horoni ndipo anapitiriza kuwapha mpaka kukafika ku Azeka ndi ku Makeda.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena