Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako Mose anauza Yehova kuti: “Anthuwa sangafike paphiri la Sinai, chifukwa inu munawachenjeza kale pamene munandiuza kuti: ‘Udule malire kuzungulira phiri ndipo muziliona kuti ndi lopatulika.’”+

  • Deuteronomo 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye anati:

      “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+

      Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri.

      Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+

      Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+

      Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena