Deuteronomo 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni,* (kuphatikizapo mzinda umene uli mʼchigwacho), mpaka kukafika ku Giliyadi, panalibe mzinda umene sitinathe kuugonjetsa. Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.+ Deuteronomo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.
36 Kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼmbali mwa chigwa cha Arinoni,* (kuphatikizapo mzinda umene uli mʼchigwacho), mpaka kukafika ku Giliyadi, panalibe mzinda umene sitinathe kuugonjetsa. Yehova Mulungu wathu anawapereka onsewo kwa ife.+
22 Yehova Mulungu wanu adzathamangitsira mitundu imeneyi kutali ndi inu, kuichotsa pamaso panu pangʼonopangʼono.+ Sadzakulolani kuti muiwononge mofulumira, kuopera kuti zilombo zakutchire zingachuluke nʼkukuwonongani.